![](https://2c717466dc25cd7041c9-8eeda6a8ca964cf210ed223dbc947813.ssl.cf2.rackcdn.com/22494780-786145818-Lazarus-Chakwera-3-100x67.jpeg)
Walifwanthamula bodza: Chakwera anamiza a Malawi pa zitukuko
Lero m’tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wavwavwaniza a Malawi ndi bodza lankunkhuniza ponena kuti boma lake lachita zitukuko za nkhani nkhani m’dziko muno zomwe ambiri akupukusa mutu opanda nyanga. Chimodzi mwa zitukuko zomwe Chakwera anati boma …